The goal of this website is to be a safe for souls website advancing Catholic thinking and education. When editing, please adhere to the Content Standards.

Some images have been enhanced for teaching purposes and may not be identical to the original artwork.

Banti Rosary Prayers

From The Work of God's Children
Jump to: navigation, search

This language is a dialect of Mundani.

This language is spoken by 34,000 people in the South West Province, Manyu Division, Mamfe and northern Fontem subdivisions, and south of Batibo in Cameroon.

Prayers that are not known in this language are shown in English until we have the complete prayer, at which time it will be shown in both languages.

Contents

+ M'DZINA LA ATATE / + The Sign of the Cross / + Signum Crucis

+ M'DZINA LA ATATE NDI + LA MWANA NDI + LA MZIMU WOYERA, AMEN.

Kumvera kwa Apostoli / The Apostles' Creed / Credo

Ine ndimvera Mulungu AtateAmphamvuzonse
amene adalenga zakumwamba ndi zapansi pano.
Ndimveranso Yesu Khristu Mwana wake yekha, Ambuye athu,
amene adayikidwa m'mimba ndi mphamvu za Mzimu Woyera
nabadwa mwa Maria Virigo,
adamsautsa kwa Ponsio Pilato.
Adampachika pamtanda, namwalira, adamuyika m'manda,
adalowa m'limbo
ndipo mkucha wake adauka kwa akufa,
adakwera kumwamba
nakhala padzanja lamanja la Mulungu Atate Amphamvuzonse.
Adzafumira komweko kudzaweruza amoyo ndi akufa.
Ndipo ndimvera Mzimu Woyera,
Eklezia Katolika Woyera,
ndimveranso kuti Oyera ayanjana,
Mulungu atikhululukira machimo,
thupi lidzauka,
ulipo moyo osatha. Amen.

Atate Athu / Our Father / Pater Noster

Matthew 6:9-13
Luke 11:2-4

Atate athu, muli mwamba,
Dzina lanu liyeretsedwe.
Ufumu wanu udze.
Kufuna kwanu kucitidwe,
Monga kumwamba choncho pansi pano.
Mutipatse lero chakudya chathu chalero.
Mutikhululukire zochimwa zathu.
Monga ifenso tikhululukira adani athu.
Musatisiye ife muchinyengo.
Koma mutipulumutse ife kwa zoyipa.
Amen.

Atate Athu / Our Father / Pater Noster

Atate athu muli m'mwamba,
dzina lanu liyeretsedwe,
ufumu wanu udze, kufuna kwanu kuchitidwe,
monga kumwamba choncho pansi pano.
Mutipatse ife lero chakudya chathu cha lero.
Mutikhululukire ife zochimwa zathu monga
ifenso tiwakhululukira adani athu,
musatisiye ife m'chinyengo
koma mutipulumutse ife ku zoyipa. Amen.

Tinione Maria / Hail Mary / Ave Maria

Tinione Maria,
Wachaulere chodzaza,
Ambuye ali nanu.
Ndinu wodala mwa akazi onse
Wodalanso ndi mwana wanu Yesu.
Maria oyera, Amayi a Mulungu,
Mutipempherere ife ochimwa Tsopano ndi panthawi yakufa kwathu.
Amen.

Tikuoneni Maria / Hail Mary / Ave Maria

Tikuoneni Maria wa chaulele chodzadza,
Ambuye ali nanu.
Ndinu odala mwa akazi onse,
Ngodalanso mwana wanu Yesu.
Maria oyera amayi a mulungu
mutipempherere ife,
Tsopano ndi pa nthawi zosatha.
Amen.

Tikuoneni Maria / Hail Mary / Ave Maria

Tikuoneni Maria wa chaulere chodzaza
Ambuye ali nanu, ndinu
wodala mwa akazi onse
ndipo ngodalanso
Mwana wanu Yesu.
Maria woyera Amayi a Mulungu
mutipempherere ife ochimwa,
tsopano ndiponso pa nthawi
ya kufa kwathu Amen.

Glory Be to the Father / Gloria Patri

Oh, My Jesus / Fatima Prayer


Oh, my Jesus, forgive us our sins. Save us from the fires of hell. Lead all souls to Heaven, especially those most in need of Your mercy.

Hail, Holy Queen / Salve Regina


Hail, Holy Queen, Mother of Mercy

Mysteries of the Rosary

The Joyful Mysteries

The Luminous Mysteries

The Sorrowful Mysteries

The Glorious Mysteries

How to Pray the Rosary

How to pray the Rosary

1. + M'DZINA LA ATATE (The Sign of the Cross / Signum Crucis)
2. Kumvera kwa Apostoli (The Apostles' Creed / Credo)
3. Atate Athu (Our Father / Pater Noster)
4. 3 Tinione Maria (Hail Mary / Ave Maria)
5. (Glory Be to the Father / Gloria Patri)
6. Announce the 1st Mystery
7. Atate Athu
8. 10 Tinione Maria
9. (Glory Be to the Father / Gloria Patri) / Oh, My Jesus
10. Announce 2nd Mystery
11. Atate Athu
12. 10 Tinione Maria
13. (Glory Be to the Father / Gloria Patri) / Oh, My Jesus
14. Announce the 3rd Mystery
15. Atate Athu
16. 10 Tinione Maria
17. (Glory Be to the Father / Gloria Patri) / Oh, My Jesus
18. Announce 4th Mystery
19. Atate Athu
20. 10 Tinione Maria
21. (Glory Be to the Father / Gloria Patri) / Oh, My Jesus
22. Announce the 5th Mystery
23. Atate Athu
24. 10 Tinione Maria
25. (Glory Be to the Father / Gloria Patri) / Oh, My Jesus
26. (Hail, Holy Queen / Salve Regina)
For the Intentions and protection of our Holy Father:
27. Atate Athu (Our Father / Pater Noster)
27. Tinione Maria (Hail Mary / Ave Maria)
27. (Glory Be to the Father / Gloria Patri)
28. + M'DZINA LA ATATE (The Sign of the Cross / Signum Crucis)

Malamulo a Mulungu / The Ten (10) Commandments

Exodus 20:2-17
Deuteronomy 5:6-21


Malamulo a Mulungu
The 10 Commandments

Usapembedze Mulungu wina koma ine ndekha.

Usatchule pachabe dzina la Ambuye Mulungu wako.

Udzikumbikira kuyeretsa tsiku lamulungu.

Lemekeza atate ako ndi amayi ako.

Usaphe.

Usachite chigololo.

Usabe.

Usachite umboni onama.

Usasirire ukwati wamwini.

Usachite kaduka ndi zinthu zamwini.

Ulemu Kwa Mulungu Kumwamba / Glory to God in the Highest / Gloria

Ulemu kwa Mulungu kumwamba,
ndipo pansi pano mtendere kwa anthu chifukwa iye akuwakonda.
Tikukuyamikani, tikukutamandani, Tikukupembedzani
tikukulemekezani, tikukuthokozani chifukwa cha
ulemu wanu waukulukulu.
Inu Ambuye Mulungu, Mfumu wakumwamba,
Mulungu Atate a mphamvu zonse.
Inunso Ambuye Yesu Khristu,
Mwana wake mmodzi yekha, Ambuye Mulungu,
Kankhosa ka Mulungu, Mwana wa Atate,
Inu amene mumachotsa machimo a anthu, mutichitire chisoni;
Inu amene mumachotsa machimo a anthu, Mverani mapemphero athu;
Inu amene mumakhala pa dzanja lamanja la Atate mutichitire chisoni.
Poti inu nokha, Yesu Khristu, ndinu woyera; Inu nokha ndinu Ambuye,
Inu nokha ndinu wopambana ndithu, limodzi ndi Mzimu Woyera, mu ulemu wa
Mulungu Atate. Amen.

The Nicene Creed / Credo

Personal tools
Namespaces
Variants
Actions
Navigation
Languages
Toolbox